Chichewa
-
Liwu la mafumu pa zochotsa anthu 1 miliyoni mu AIP
Mafumu apereka maganizo osiyanasiyana pa ganizo la boma lochotsa maina 1 miliyoni mu pulogalamu ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo…
Read More » -
Boma likugwiritsa K3 biliyoni pothandiza ochotsa mimba
Dziko la Malawi likugwiritsa ntchito pafupifupi K3 biliyoni pa chaka popereka thandizo kwa amayi amene anachotsa mimba pogwiritsa ntchito njira…
Read More » -
Gogo athawa m’mudzi mwake
Abale a gogo Binwell Chabwera amene adathawitsidwa pomuganizira kuti adapha mdzukulu wake m’matsenga anenetsa kuti iwo sakufunanso kuona gogoyo. Gogo…
Read More » -
Zaka ziwiri kwa akuba pa foni
Bwalo la Nsanje Third Grade Magistrate lalamula amuna awiri kukagwira ukaidi kwa miyezi 24 atawapeza wolakwa pa mlandu woba mafoni.…
Read More » -
Alimi akhutira ndi chionetsero
Alimi ena amene afika ku chionetsero cha ulimi chimene nduna ya za malimidwe a Sam Kawale adatsegulira dzulo mu mzinda…
Read More » -
Aphungu akwangula zokambirana
Pamene aphungu a Nyumba ya Malamulo amayembekezeka kukwangula zokambirana zawo dzulo, mkulu wa bungwe loona za ufulu wa anthu la…
Read More » -
Maneb itulutsa maina aophunzira 10 okhoza kwambiri
Bungwe la za mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) latulutsa mndandanda wa ophunzira 10 amene achita bwino kwambiri pa…
Read More » -
Ng’anga zaithina itakanika kudzutsa munthu wakufa
Ng’anga ina ku Balaka yapereka chindapusa cha K90 000 kupewa kukaseweza miyezi 15 imene adamugamula atapezeka wolakwa pa mlandu woti…
Read More » -
Misika ya Admarc siyitsegulidwa msanga
Nduna ya za malimidwe a Sam Kawale ati kampani yogula mbewu ya Admarc siyitsegulidwa kuti iyambe kugula mbewu pokhapokha anthu…
Read More » -
Zaka 59 pa ufulu tapindulanji
Kadaulo pa ndale a George Phiri ati palibe chifukwa chomveka choti dziko la Malawi lizikondwerera ufulu wodziimirira palokha chifukwa m’zambiri…
Read More »