Chichewa
-
Imfa ya wa kabanza
Anthu okwiya m’taunishipi ya Machinjiri mu mzinda wa Blantyre aphwanya mazenera ndi zitseko za polisi yaing’ono ya Nanthoka ndi kuotcha…
Read More » -
A Joyce Banda ndi amayi okhawo omwe akufuna kudzapikisana nawo
Pofika dzuro m’mawa, atsogoleri 14 ndiwo anatenga makalata kuchokera ku bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) ofuna kudzapikisana nawo pa…
Read More » -
Amayi apatsidwe mwayi pa ndale
Mabungwe a Oxfam ndi Women and Legal Resource Centre (WOLREC) akuthandiza amayi, achinyamata ndi anthu aulumali omwe akufuna kudzapikisana nawo…
Read More » -
Akhazikitsa ndondomeko zoletsaandale kukopa ovota ndi katundu
Mkulu wa ofesi yoona m’mene zipani za ndale zimagwirira ntchito zawo, a Kizito Tenthani, akhala akukumana ndi atsogoleri a zipani…
Read More » -
Achinyamata akufuna maudindo
Mtsogoleri wa bungwe la Youth and Society a Charles Kajoloweka asindika kufunika kokhazikitsa malamulo okakamiza boma kuti lizipereka maudindo ena…
Read More » -
Women yakhazikitsa manifesito
Akatswiri omenyera ufulu wa amayi akuti manifesito ya amayi ndi chida cha mphamvu chosinthira moyo wawo pa ndale m’dziko muno.…
Read More » -
Kuunika za Simatimatiki
Mtsutso wabuka pakati pa zipani zotsutsa boma ndi bungwe loyendetsa zisankho m’dziko muno la Malawi Electoral Commission (MEC) pa nkhani…
Read More » -
Apolisi akonzeka kuthanandi ziwawa zokhudza ndale
KANDANI NGWIRA ndi BRIGHT KUMWENDA Apolisi akuti apereka chitetezo chokwanira m’misonkhano yokopa anthu, povota komanso potulutsa zotsatira za chisankho cha…
Read More » -
Wakuba ufa ndi makala agamulidwa zaka 4
Bambo Cosmas Chiwambo, a zaka 22, omwe amachokera m’mudzi mwa Mwamadi kwa T/A Chikumbu m’boma la Mulanje, alamulidwa kuti akakhale…
Read More » -
Amanga oba zitsulo pa mlatho
Apolisi m’boma la Mulanje atsekera m’chitokosi abambo anayi powaganizira kuti adaba zitsulo za pa mlatho wopezeka m’dera la kummwera cha…
Read More »