Chichewa
-
‘Si ife oyendayenda’
Amayi amene ali ndi mwana kapena ana koma si ali pa banja si mahule, momwe ena amaganizira, watero mlembi komanso…
Read More » -
Apempha kafukufuku pa CDF
Pomwe chiwerengero cha anthu maka abambo odzipha chikupitirira kukwera m’dziko nacho chiwerengero cha achinyamata makamaka omwe ali sukulu za ukachenjede…
Read More » -
6 July ili ku BNS
Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu apempha Amalawi amene akudzapita ku chisangalalo choti dziko lino lakwanitsa zaka 61 lili…
Read More » -
Achinyamata sakufooka, sakubwerera mmbuyo
Achinyamata, omwe adzapikitsana nawo pa zisankho za makhansala ndi a phungu a Nyumba ya Malamulo pa 16 Sepitembala, maso awo…
Read More » -
Namiwa alira: dzikoli lafika apa?
Patangotha masiku atatu akuluakulu a nthambi za chitetezo atasankha atsogoleri a za chitetezo pomwe dziko lino likukonzekera Chisankho Chachikulu pa…
Read More » -
Imfa ya wa kabanza
Anthu okwiya m’taunishipi ya Machinjiri mu mzinda wa Blantyre aphwanya mazenera ndi zitseko za polisi yaing’ono ya Nanthoka ndi kuotcha…
Read More » -
A Joyce Banda ndi amayi okhawo omwe akufuna kudzapikisana nawo
Pofika dzuro m’mawa, atsogoleri 14 ndiwo anatenga makalata kuchokera ku bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) ofuna kudzapikisana nawo pa…
Read More » -
Amayi apatsidwe mwayi pa ndale
Mabungwe a Oxfam ndi Women and Legal Resource Centre (WOLREC) akuthandiza amayi, achinyamata ndi anthu aulumali omwe akufuna kudzapikisana nawo…
Read More » -
Akhazikitsa ndondomeko zoletsaandale kukopa ovota ndi katundu
Mkulu wa ofesi yoona m’mene zipani za ndale zimagwirira ntchito zawo, a Kizito Tenthani, akhala akukumana ndi atsogoleri a zipani…
Read More » -
Achinyamata akufuna maudindo
Mtsogoleri wa bungwe la Youth and Society a Charles Kajoloweka asindika kufunika kokhazikitsa malamulo okakamiza boma kuti lizipereka maudindo ena…
Read More »