Chichewa
-
Akachasu nawo akulira ndi kukwera kwa shuga
Mwina n’kumaona ngati amene amakonda za tseketseke monga tiyi ndi makeke okha ndi amene akulira ndi kusowa komanso kukwera mtengo…
Read More » -
Kusamvana pa mwambo wokumbukira Chilima
Mwambo wokumbukira yemwe adali mtsogoleri wakale wa dziko lino a Saulos Chilima uchitika Lachiwiri likudzali kwawo ku Nsipe komwe thupi…
Read More » -
Awachotsa pa mpando atayendera a Bushiri
Kadaulo pa ndale kuno ku Malawi a George Chaima komanso wa ku South Africa a Dr Zwakala ati payenera kukhala…
Read More » -
‘Bweretsani zakudya osati Sim-card ku ndende’
Mkulu wa asilikali pa ndende ya Zomba Central Prison a Austin Nyoni ati m’malo mowotcha kapena kuphwanya ma foni ndima…
Read More » -
Mafumu alankhula pa chigamulo cha khoti pa CDF
Chigamulo cha khothi choletsa aphungu kuyendetsa ndalama zachitukuko za Constituency Development Fund (CDF) chapereka maganizo osiyana pakati pa anthu. Khoti…
Read More » -
Banja ndalilephera
Anatche, muli bwanji? Ine mavuto.Banja ndidalikondetsetsa koma ndikuona ngati ndililephera. Ndili pa banja ndipo tili ndi ana awiri. Wina wamaliza…
Read More » -
Achenjeza obwereketsa galimoto: Kuli mbanda
Bambo wina yemwe dzina lake ndi Emmanuel Davie, ali m’manja mwa apolisi pomuganizira kuti adanamiza anthu kuti ndi msilikali wa…
Read More » -
‘Smartmatic’ yautsa mapiri pa chigwa
Njira yamakina a makono oyendetsera zisankho otchedw Elections Monitoring Devices (EMD) amene akutchuka ndi dzina la kampani yak u Netherlands…
Read More » -
Polisi yati mitima ikhale mmalo
Mkulu wa apolisi Mayi Me r l y ne Yol amu atsimikizira zipani za ndale ndi mabungwe oima paokha kuti…
Read More » -
DPP, MCP alozana zala
Zipani za MCP ndi DPP zikulozana zala pa amene adayambitsa ziwawa zimene zidachitika ku mapeto a sabata yatha ku Mponela…
Read More »