Chichewa
-
Thandizo sakakamiza, watero Namadingo
Pomwe chiyembekezo cha mafumu cha anthu a ku Mangochi chili mmwamba kuti maambulansi amene adafa ndipo woimba Patience Namadingo anadzipereka…
Read More » -
‘Dekhani za a bushiri’
Oimira anthu pa milandu, a Jai Banda komanso a Khwima Mchizi apempha Amalawi kuti adekhe pa mlandu omwe mneneri wa…
Read More » -
Aotcha makilogalamu a chamba
Bwalo la milandu ku Salima lagamula kutentha chamba chokwana makilogalamu 576.68 komanso kuti mwini wake, a Adam Likagwa a zaka…
Read More » -
Apempha zipani kuthandiza a ulumali
Mkulu wa bungwe la Disability HIV/Aids Trust yomwe ndi nthambi ya Federation of Disability Organizations in Malawi (Fedoma) a David…
Read More » -
Kwadza zipani zina za ndale
Pomwe masiku a chisankho akusunthira ku chitseko, zipani zina za ndale zitatu zalembetsa ku ofesi ya mlembi wa zipani za…
Read More » -
Ena ayamba kukolola chimanga chosauma
Mbala zavuta mpaka alimi ena ayamba kukolola dowe kuopa kuti akadikira nyengo yoyenera kukolola adzapeza mapesi okhaokha m’munda. Nduna ya…
Read More » -
Dausi aseketsa aphungu
Zitsuzo sizimamuthera phungu wa m’dera lapakati m’boma la Mwanza a Nicholas Dausi. A Dausi adadzuka pa mpando wawo m’Nyumba ya…
Read More » -
Anthu alembetsa mwaunyinji—MEC
Bungwe loyendetsa zisankho la MEC lati anthu chiwerengero cha anthu omwe alembetsa kuti adzavote pa Chisankho Chachikulu cha pa 16…
Read More » -
Amuna anga matama thooo!
Azakhali, zili kwathu simungazimvetse. Ife tonse tili pa ntchito. Tonse timalandira ndalama zokwanira ndithu. Komwe ndalama za amuna anga zimapita…
Read More » -
‘Samalani m’masamba a mchezo’
Mkulu wa bungwe loteteza ufulu wa ana ndi achinyamata a MacBain Mkandawire wapempha Amalawi kuti azigwiritsa ntchito masamba a mchezo…
Read More »