Chichewa
-
America iyimika thandizo
Kadaulo wa mgwirizano wa mabungwe a zaumoyo la Malawi Health Equity Network (Mhen) a George Jobe ati zomwe lachita dziko…
Read More » -
Mtengo wa chimanga wapenga
Kusowa kwa chimanga m’misika ya Admarc kwapereka danga kwa mavenda ogulitsa chimangacho kuti akame Amalawi omwe akulira kale ndi njala…
Read More » -
Ati tikhwimire mwana
Ndili pa banja ndipo tili ndi ana angapo. Banja lathu ndi loopa Mulungu. Ndipo tonse ndi atsogoleri ku mpingo wathu.…
Read More » -
Banja lituluka pa belo
Bwalo la milandu mu mzinda wa Blantyre, Lachisanu lidapereka belo kwa mayi Linda Chitala ndi amuna awo a Macferson Chitala…
Read More » -
Akuluakulu 6 amangidwa m’masiku awiri
Akuluakulu omwe akudzimva fungo la milandu akuyenera kuyenda cheucheu kaamba koti unyolo wathyola mpanda ku polisi ndipo ukuika manja kumbuyo…
Read More » -
APM adzudzula Chakwera
Kadaulo pa ndale a George Phiri wati akugwirizana ndi zimene adanena mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika kuti…
Read More » -
Ndimamufuna kwambiri
Anatchereza M’mudzi mwathu mudabwera mtsikana wina wake yemwe ndidakondweretsedwa naye. Ndidachita machawi kumufunsila ndi kumuuza kuti ndimamukonda koma sadandiyankhe. Mwa…
Read More » -
Amayi ayiphula ndi a Mpinganjira
Lachinayi sabata yatha lidayamba monga tsiku ngati lililonse kwa mayi Mary Chikaonda omwe amaotcha tchipisi komanso zipalasilo ndi mitu ya…
Read More » -
A Chakwera aonjezera nduna…Zachoka pa 27 kufika pa 31
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati asintha zina mwa nduna zawo n’kuonjezera chiwerengero cha nduna ndi achiwiri awo…
Read More » -
2024 Amalawi adaziona
Chaka cha 2024 ndi china mwa zaka zomwe Amalawi sadzaiwala kaamba ka ziyangoyango zomwe adadutsamo mpaka ena kumalingalira za zionetsero.…
Read More »