Chichewa
-
test1
Malawi Election Coverage 2025 Live vote entry and results Enter Votes Region/District: Jane Banda: Joseph Mphatso: Chikondi Tembo: Submit Votes…
Read More » -
Ana 1 487 abadwa pa Khrisimasi
Ku Dowa kudabadwa ana 71 tsiku la Khrisimasi chaka chino. M’dziko lonseli mudabadwa ana 1 487 pa tsiku lokumbukira kubadwa…
Read More » -
Ndalama zawo sizikulondeka
Zikomo, Anatche, ine zandivuta koopsa. Ndili pa banja ndipo ndili ndi ana atatu. Banja lathu ndi losalongosoka. Ndanena chonchi chifukwa…
Read More » -
Ankadzitama ku chipinda
Anatchereza, ine ndathedwa nzeru. Ndili pa banja ndipo ndili ndi ana atatu. Tonse timagwira ntchito. Ndisanayambe Anatche, ndiseke kaye. He…
Read More » -
Oyendayenda achichepere Akupha msika wa amkhalakale
Amayi oyendayenda sakukondwa ndi atsikana achichepere omwe akumapezeka m’malo azisangalalo popeza akuwalanda makasitomala. Izi zikuchititsa kuti amayiwa, amene amatchaja K10…
Read More » -
Anyumwa ndi zitupa za unzika m’nkhokwe
Kudali mpungwepungwe Lachitatu pomwe aphungu a mbali yotsutsa boma adakapeza zitupa za unzika ku nkhokwe yosungirako chimanga ya National Food…
Read More » -
‘Osatengeka ndi mabokosi’
Anthu ena a m’dera la kummwera mu mzinda wa Blantyre achenjeza ovota m’deralo ngakhalenso dziko la Malawi kuti akhale osamala…
Read More » -
‘Menopause’ ikuwazunguza?
Azakhali, Zikuonetsa kuti akazi anga atopa nane. Ine ndi akazi anga tonse tili m’zaka za m’ma 30 ndipo tikusiyana ndi…
Read More » -
Akundizunza ku chikamwini
Azakhali, Ndine mayi wa zaka 24. Ndidakwatiwa ndi mwamuna yemwe ndidamukonda, ndilibe naye mwana chifukwa nditatenda pathupi, mimba idapita malo…
Read More » -
Ofuna utsogoleri wa UTM apereka zikalata
Pamaoneka gwedegwede wokhudza msonkhano waukulu wa chipani cha UTM koma tsopano zaoneka kuti mutu wa konvenshoniyo ilikoliko pa 17 November…
Read More »