Nkhani
-
Akuti mtima mmalo, chitetezo chilipo pa zisangalalo
Nduna ya za chitetezo cha m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma ati unduna wawo wakhwimitsa chitetezo m’nyengo ya zisangalalo za Khrisimasi…
Read More » -
DPP idyera Khrisimasi m’khoti
Woweruza ku bwalo la milandu lalikulu ku Lilongwe a Justice Howard Pemba ati adzapereka chigamulo chawo pa 26 December 2023…
Read More » -
Mchitidwe wogona ndi ana ukukula kwambiri
Pamene bwalo lina ku Zomba m’sabata yangothayi lidagamula kuti mphunzitsi wina ndi wosalakwa pa mlandu wogwiririra mwana wophunzira pasukulu ya…
Read More » -
Ziphaso zitheka pofika 2025
Nduna ya za chitetezo cha m’dziko a Ken Zikhale Ng’oma ati pofika m’chaka cha 2025 pomwe Amalawi adzaponye voti ya…
Read More » -
Kwafa bulu ku DPP
Mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Peter Mutharika wauza mamembala omwe sakumumvera m’chipanicho kuti achoke asaononge chipani. A…
Read More » -
Mfumu yadzikhweza ndi za fetereza wa AIP
Amfumu a Chidzalo a zaka 71 omwe dzina lawo ndi a Moffat Lamulani Mlenga a m’boma la Dowa adzikhweza pothawa…
Read More » -
Amanga 10 pa mkangano wa ufumu
Apolisi ku Ntchisi amanga anthu 10 a m’mudzi mwa Kanyenda kwa T/A Kalumo potsatira mkangano wa ufumu pakati pa a…
Read More » -
Mitala iphetsa
Mayi wa zaka 19 wadzipha ku Kasungu atazindikira kuti mwamuna yemwe adakwatirana naye pokhulupirira kuti banja lake loyamba lidatha ndi…
Read More » -
Chiyembekezo chakwera ndi mawu a Chakwera
Pakati pa usiku wa Lachitatu sabata yatha, ndalama ya kwacha idatsika mphamvu ndi K44 pa K100 iliyonse. Izi zachititsa kuti…
Read More » -
chiwanda chophana chavuta
Chiwanda chachilendo chophana m’mabanja chalowerera moti mwezi umodzi okha, bambo wina ku Zomba adapha mkazi wake, banja lina ku Chiradzulu…
Read More »