Nkhani
-
Miyezi 30 kwa ogona ndi ng’ombe
Bwalo la Chitipa Senior Resident Magistrate, Lolemba pa 14 July 2025, lidagamula bambo wina wa zaka 24 a James Mtambo,…
Read More » -
Adandaula za nyumba ya chisoni
Anthu okhala m’dera la Lisungwi m’boma la Neno adandaula ndi kusagwira ntchito kwa nyumba ya chisoni. Nyumba ya chisoni ya…
Read More » -
Amanga womuganizira kuba chimanga
Bwalo la First Grade Magistrate ku Thyolo masiku apitawa lidagamula bambo Mphatso Mateyu, omwe amachokera m’mudzi mwa Changata, m’dera la…
Read More » -
Kampeni iyamba lolemba
Chisankho cha 2025 chifika gawo lina Lolemba likudzali pomwe bungwe loyendetsa zisankho la MEC lidzakhazikitse misonkhano yokopa anthu. Malingana ndi…
Read More » -
Akufuna boma lichitepo kanthu pa za zigandanga
Akadaulo oimira magulu osiyanasiyana ati boma likuyenera kuchitapo kanthu pa za zigandanga za zikwanje zomwe zakhala zikusokoneza zionetsero osati kungolankhulapo…
Read More » -
‘Si ife oyendayenda’
Amayi amene ali ndi mwana kapena ana koma si ali pa banja si mahule, momwe ena amaganizira, watero mlembi komanso…
Read More » -
Apempha kafukufuku pa CDF
Pomwe chiwerengero cha anthu maka abambo odzipha chikupitirira kukwera m’dziko nacho chiwerengero cha achinyamata makamaka omwe ali sukulu za ukachenjede…
Read More » -
6 July ili ku BNS
Nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu apempha Amalawi amene akudzapita ku chisangalalo choti dziko lino lakwanitsa zaka 61 lili…
Read More » -
Namiwa alira: dzikoli lafika apa?
Patangotha masiku atatu akuluakulu a nthambi za chitetezo atasankha atsogoleri a za chitetezo pomwe dziko lino likukonzekera Chisankho Chachikulu pa…
Read More » -
Imfa ya wa kabanza
Anthu okwiya m’taunishipi ya Machinjiri mu mzinda wa Blantyre aphwanya mazenera ndi zitseko za polisi yaing’ono ya Nanthoka ndi kuotcha…
Read More »