Nkhani

  • Apempha zipani kuthandiza a ulumali

    Mkulu wa bungwe la Disability HIV/Aids Trust yomwe ndi nthambi ya Federation of Disability Organizations in Malawi (Fedoma) a David…

    Read More »
  • Kwadza zipani zina za ndale

    Pomwe masiku a chisankho akusunthira ku chitseko, zipani zina za ndale zitatu zalembetsa ku ofesi ya mlembi wa zipani za…

    Read More »
  • Ena ayamba kukolola chimanga chosauma

    Mbala zavuta mpaka alimi ena ayamba kukolola dowe kuopa kuti akadikira nyengo yoyenera kukolola adzapeza mapesi okhaokha m’munda. Nduna ya…

    Read More »
  • Dausi aseketsa aphungu

    Zitsuzo sizimamuthera phungu wa m’dera lapakati m’boma la Mwanza a Nicholas Dausi. A Dausi adadzuka pa mpando wawo m’Nyumba ya…

    Read More »
  • Anthu alembetsa mwaunyinji—MEC

    Bungwe loyendetsa zisankho la MEC lati anthu chiwerengero cha anthu omwe alembetsa kuti adzavote pa Chisankho Chachikulu cha pa 16…

    Read More »
  • Amuna anga matama thooo!

    Azakhali, zili kwathu simungazimvetse. Ife tonse tili pa ntchito. Tonse timalandira ndalama zokwanira ndithu. Komwe ndalama za amuna anga zimapita…

    Read More »
  • ‘Samalani m’masamba a mchezo’

    Mkulu wa bungwe loteteza ufulu wa ana ndi achinyamata a MacBain Mkandawire wapempha Amalawi kuti azigwiritsa ntchito masamba a mchezo…

    Read More »
  •  America iyimika thandizo

    Kadaulo wa mgwirizano wa mabungwe a zaumoyo la Malawi Health Equity Network (Mhen) a George Jobe ati zomwe lachita dziko…

    Read More »
  • Mtengo wa chimanga wapenga

     Kusowa kwa chimanga m’misika ya Admarc kwapereka danga kwa mavenda ogulitsa chimangacho kuti akame Amalawi omwe akulira kale ndi njala…

    Read More »
  • Ati tikhwimire mwana

    Ndili pa banja ndipo tili ndi ana angapo. Banja lathu ndi loopa Mulungu. Ndipo tonse ndi atsogoleri ku mpingo wathu.…

    Read More »
Back to top button