Nkhani
-
Akundizunza ku chikamwini
Azakhali, Ndine mayi wa zaka 24. Ndidakwatiwa ndi mwamuna yemwe ndidamukonda, ndilibe naye mwana chifukwa nditatenda pathupi, mimba idapita malo…
Read More » -
Ofuna utsogoleri wa UTM apereka zikalata
Pamaoneka gwedegwede wokhudza msonkhano waukulu wa chipani cha UTM koma tsopano zaoneka kuti mutu wa konvenshoniyo ilikoliko pa 17 November…
Read More » -
AIP yadza nzakenso
Unduna wa za malimidwe udati alimi ayamba kugula zipangizo za ulimi zotsika mtengo sabata yomwe ikuthayi koma Tamvani wapeza kuti…
Read More » -
Mavuto a mnanu kwa osamutsidwa
Awa ndi mayi Margaret Julius. Madzi atasefukira m’mudzi mwawo mwa Chililamadzi ku Makhanga m’boma la Nsanje mwezi wa March chaka…
Read More » -
Mnzanga akusokoneza banja langa
Ndili pa banja ndipo ndili ndi ana. Ana anga onse amapita sukulu za pa mwamba chifukwa choti bambo awo amawalipirira.…
Read More » -
NRB ilembere opanda ma ID
Pamene kalembera wa amene akufuna kudzavota pa Chisankho Chachikulu cha pa 16 September chaka cha mawa ali mkati, anthu amene…
Read More » -
A Kaliati akadali m’manja mwa apolisi
Mlembi wamkulu wa chipani cha UTM mayi Patricia Kaliati akhoza kukhala m’chitokosi ku mapeto kwa sabata ino m’chitokosi kuchokera pomwe…
Read More » -
Ndidatseketsa mowabisira
Azakhali, Mutu wanga waima chifukwa ndazunguzika ndi mavuto omwe ndikukumana nawo. Ine ndi mayi wa ana atatu ndipo ndili pa…
Read More » -
Kalembera wa chisankho ayamba lolemba lomweli
Kalembera wa chisankho cha 2025 ayamba Lolemba likudzali pomwe zipani zakangalika kumema anthu ozitsatira kuti akalembetse mwa unyinji kuti adzakhale…
Read More » -
Kamangila wakwekwesa jaji
Woweruza milandu ku khoti la za chuma a Kenan Manda ati mmodzi mwa maloya odziwika a Alexious Kamangila awapepese kaamba…
Read More »