Chichewa
-
Akwizinga ‘wogwirira’ wamisala
Apolisi ya Kanengo ku Lilongwe anjata bambo wa zaka 46 Nelson Chiudzu pomuganizira kuti adagwirira mai wa zaka 49…
Read More » -
‘Tidadziwana tili ana’
Mtolankhani wa za masewero ku wailesi ya Voice of Livingstonia (VOL) Sylvester Siloh Kapondera adakumana ndi wokondedwa wake Annie Chivunga…
Read More » -
Khama ndiye yankho poweta ng’ombe zamkaka
Kuchionetsero cha zaulimi cha National Agriculture Fair ku Trade Fair Grounds mumzinda wa Blantyre, Peacewell Edward Mlanga, wochokera kwa Senior…
Read More » -
Kusanthula khansa ya m’mawere
Petani Mtonga, wachiwiri kwa mkulu wa nthambi ya matenda a khansa kuchipatala cha Queen Elizabeth mumzinda wa Blantyre wati matenda…
Read More » -
Chisamaliro choyenera cha ng’ombe za mkaka
Ngakhale alimi ambiri a ng’ombe za mkaka amabwekera kuti akupeza phindu ku ulimiwu, Jacob Mwasinga, mlangizi wa ziweto ku Mzuzu…
Read More » -
Osauka alibe mawu
Kwa zaka 12, ena mwa omwe akuwaganizira milandu yakupha akadali pa alimandi m’ndende podikira chilungamo pa milandu yoganiziridwa…
Read More » -
Chilengedwe chikubwerera ku Mangochi
Sungapirire mfuu wa mbalame—wopokerezedwa bwino ngati nyimbo m’mitengo yachilengedwe m’boma la Mangochi. Nkhalango yachilengedwe ya m’mudzi mwa Chembe m’boma…
Read More » -
Milandu yachepa ku Blantyre
Milandu yosiyanasiyana mu mzindawa Blantyre yatsika kuchoka pa 328 mu February chaka chatha kufika pa 204 mwezi omwewo chaka…
Read More » -
Maphunziro alowa libolonje
Mphunzitsimmodzi, ana 110 Komaaphunzitsi 10 000 akusowantchito Dziko la Malawi lalephera kukwaniritsa loto lake loti pofika chaka chino, mphunzitsi mmodzi…
Read More » -
Ine ayi, Dausi wakana Chaponda
Zomwe zachitika ku bwalo la mirandu ku Lilongwe m’sabatayi zalephera kupherezera mwambi woti khoswe akakhala pa mkhate sapheka. Khwimbi…
Read More » -
Ulendo wa chisankho wapsa
Zipani zina zati bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) liyenera kukwaniritsa zomwe lidalonjeza sabata yatha kuti chisankho cha…
Read More » -
Zikhulupiriro zikufalitsa kolera—unduna
Unduna wa zaumoyo wati zikhulupiriro ndizo zikuchititsa kuti chiwerengero odwala kolera chizikwera. Koma bungwe la United Nations Children’s Fund (Unicef)…
Read More » -
Chitetezo chaphwasuka
Chitetezo chaphwasuka. Anthu akuberedwa, kumenyedwa ndi kuchitidwa zachipongwe zambiri. Akaitanitsa apolisi akuti akumatenga nthawi kuti abwera ndipo nthawi zina sabwera.…
Read More » -
Kolera yaluma mano
Nthenda ya kolera imene idayamba ngati njerengo mwezi wa November chaka chatha, ikukwererabe moti kuchoka Lachisanu sabata yatha chiwerengero…
Read More » -
Kalembera wa mafoni aima
Boma laimitsa kalembera wa lamya za m’manja yemwe nthambi yoyendetsa ntchito za mauthenga ya Malawi Communications Regulatory Authority (Macra) idakhazikitsa…
Read More » -
Chilimikani pa ulimi—Kazembe
Malinga ndi ng’amba imene yasautsa m’madera ambiri m’dziko lino, wachiwiri kwa kazembe wa limodzi mwa maiko a ku Ulaya la…
Read More » -
MEC ikufunakusinthatsiku la chisankho
Pavuta kuti chisankho chichoke mwezi wa May kupita September monga bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lidapemphera komitiya…
Read More » -
Osinthasintha zipani ngosadalilika—Akadaulo
Andale osinthasintha zipani ndi osadalilika, ndipo amachita izi chifukwa cha dyera, atero akadaulo ena a zandale. Koma ena mwa andalewo…
Read More » -
Kwadza kaundula wa foni za m’manja
Eni lamya za m’manja m’dziko muno akuyenera kulowa m’kaundula wa umwini wa lamya zawo kuti azitha kugwiritsa ntchito lamya zawozo,…
Read More » -
NRB ionjezera masiku otengera zitupa
Ntchito yopereka zitupa za unzika kwa anthu a m’maboma 15 m’dziko muno, imene imayenera kutha dzulo ayionjezera m’boma la Blantyre,…
Read More »